Yohane 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu adzakuchotsani m’sunagoge.+ Ndipo nthawi ikubwera pamene aliyense wakupha inu adzaganiza kuti wachita utumiki wopatulika kwa Mulungu.+ Machitidwe 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano Saulo anayamba kuzunza mpingo mwankhanza. Anali kulowa m’nyumba ndi nyumba, ndi kukokera panja amuna ndi akazi omwe, n’kukawaponya m’ndende.+ 1 Akorinto 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ineyo ndine wamng’ono kwambiri+ mwa atumwi onse, ndipo si ine woyenera kutchedwa mtumwi, chifukwa ndinazunza+ mpingo wa Mulungu. Agalatiya 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munamva ndithu zimene ndinali kuchita ndili m’Chiyuda,+ kuti ndinkazunza kwambiri+ mpingo wa Mulungu ndi kupitirizabe kuuwononga.+ 1 Timoteyo 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anatero ngakhale kuti kale ndinali wonyoza Mulungu, wozunza anthu ake+ ndiponso wachipongwe.+ Komabe anandichitira chifundo+ chifukwa ndinali wosadziwa+ ndi wopanda chikhulupiriro.
2 Anthu adzakuchotsani m’sunagoge.+ Ndipo nthawi ikubwera pamene aliyense wakupha inu adzaganiza kuti wachita utumiki wopatulika kwa Mulungu.+
3 Tsopano Saulo anayamba kuzunza mpingo mwankhanza. Anali kulowa m’nyumba ndi nyumba, ndi kukokera panja amuna ndi akazi omwe, n’kukawaponya m’ndende.+
9 Ineyo ndine wamng’ono kwambiri+ mwa atumwi onse, ndipo si ine woyenera kutchedwa mtumwi, chifukwa ndinazunza+ mpingo wa Mulungu.
13 Munamva ndithu zimene ndinali kuchita ndili m’Chiyuda,+ kuti ndinkazunza kwambiri+ mpingo wa Mulungu ndi kupitirizabe kuuwononga.+
13 Anatero ngakhale kuti kale ndinali wonyoza Mulungu, wozunza anthu ake+ ndiponso wachipongwe.+ Komabe anandichitira chifundo+ chifukwa ndinali wosadziwa+ ndi wopanda chikhulupiriro.