Yohane 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tiyenera kugwira ntchito za iye amene anandituma ine kudakali masana.+ Usiku+ ukubwera pamene munthu sangathe kugwira ntchito. Akolose 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pitirizani kuyenda mwanzeru pochita zinthu ndi anthu akunja,*+ ndipo muzigwiritsa ntchito bwino nthawi yanu.*+
4 Tiyenera kugwira ntchito za iye amene anandituma ine kudakali masana.+ Usiku+ ukubwera pamene munthu sangathe kugwira ntchito.
5 Pitirizani kuyenda mwanzeru pochita zinthu ndi anthu akunja,*+ ndipo muzigwiritsa ntchito bwino nthawi yanu.*+