2 Akorinto 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho ngati aliyense ali wogwirizana ndi Khristu, iye ndi cholengedwa chatsopano.+ Zinthu zakale zinatha,+ ndipo pali zatsopano.+ Aefeso 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti ndife ntchito ya manja ake,+ ndipo tinalengedwa+ mogwirizana+ ndi Khristu Yesu kuti tichite ntchito zabwino,+ zimene Mulungu anakonzeratu+ kuti tiyendemo.
17 Choncho ngati aliyense ali wogwirizana ndi Khristu, iye ndi cholengedwa chatsopano.+ Zinthu zakale zinatha,+ ndipo pali zatsopano.+
10 Pakuti ndife ntchito ya manja ake,+ ndipo tinalengedwa+ mogwirizana+ ndi Khristu Yesu kuti tichite ntchito zabwino,+ zimene Mulungu anakonzeratu+ kuti tiyendemo.