Aroma 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Motero tinaikidwa m’manda+ pamodzi ndi iye pobatizidwa mu imfa yake, kuti monga mmene Khristu anaukitsidwira kwa akufa mwa ulemerero wa Atate,+ ifenso tiziyenda m’moyo watsopano.+ Agalatiya 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti kudulidwa kapena kusadulidwa si kanthu,+ koma chofunika ndi kukhala wolengedwa mwatsopano.+
4 Motero tinaikidwa m’manda+ pamodzi ndi iye pobatizidwa mu imfa yake, kuti monga mmene Khristu anaukitsidwira kwa akufa mwa ulemerero wa Atate,+ ifenso tiziyenda m’moyo watsopano.+
15 Pakuti kudulidwa kapena kusadulidwa si kanthu,+ koma chofunika ndi kukhala wolengedwa mwatsopano.+