Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Akorinto 5:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho ngati aliyense ali wogwirizana ndi Khristu, iye ndi cholengedwa chatsopano.+ Zinthu zakale zinatha,+ ndipo pali zatsopano.+

  • Agalatiya 6:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pakuti kudulidwa kapena kusadulidwa si kanthu,+ koma chofunika ndi kukhala wolengedwa mwatsopano.+

  • Aefeso 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kutinso mogwirizana ndi chuma+ cha ulemerero wake, akuloleni kuti munthu wanu wamkati+ akhale wamphamvu, mwa mphamvu ya mzimu wake,+

  • Akolose 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 ndipo muvale umunthu watsopano+ umene Mulungu amapereka, kutanthauza kuti mwa kudziwa zinthu molondola, muchititse umunthu wanu kukhala watsopano mogwirizana ndi chifaniziro+ cha Mulungu.

  • 1 Yohane 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tikudziwa kuti tinali akufa koma tsopano ndife amoyo+ chifukwa timakonda abale athu.+ Amene sakonda m’bale wake ndiye kuti adakali mu imfa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena