1 Yohane 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amene amakonda m’bale wake ndiye kuti ali m’kuunika,+ ndipo palibe chimene chingamukhumudwitse.+