Akolose 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndipo muvale umunthu watsopano+ umene Mulungu amapereka. Umunthu watsopano umenewu ndi wopangidwa mogwirizana ndi chifaniziro cha Mulungu.+ Choncho pamene mukudziwa Mulungu molondola, pitirizani kuchititsa umunthu wanu kukhala watsopano. Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:10 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2017, tsa. 22 Galamukani!,7/8/1995, tsa. 17 Nsanja ya Olonda,11/1/1990, ptsa. 5-64/15/1990, tsa. 274/1/1990, ptsa. 16-202/1/1989, tsa. 5 Mawu a Mulungu, ptsa. 176-179
10 ndipo muvale umunthu watsopano+ umene Mulungu amapereka. Umunthu watsopano umenewu ndi wopangidwa mogwirizana ndi chifaniziro cha Mulungu.+ Choncho pamene mukudziwa Mulungu molondola, pitirizani kuchititsa umunthu wanu kukhala watsopano.
3:10 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2017, tsa. 22 Galamukani!,7/8/1995, tsa. 17 Nsanja ya Olonda,11/1/1990, ptsa. 5-64/15/1990, tsa. 274/1/1990, ptsa. 16-202/1/1989, tsa. 5 Mawu a Mulungu, ptsa. 176-179