Yohane 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndithudi ndikukuuzani, Iye wakumva mawu anga ndi kukhulupirira amene anandituma ine ali nawo moyo wosatha,+ ndipo salowa m’chiweruzo koma wachoka ku imfa, waolokera ku moyo.+ Aroma 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti chilamulo+ cha mzimu+ umene umapatsa moyo+ mwa Khristu Yesu chakumasulani+ ku chilamulo cha uchimo ndi cha imfa.+
24 Ndithudi ndikukuuzani, Iye wakumva mawu anga ndi kukhulupirira amene anandituma ine ali nawo moyo wosatha,+ ndipo salowa m’chiweruzo koma wachoka ku imfa, waolokera ku moyo.+
2 Pakuti chilamulo+ cha mzimu+ umene umapatsa moyo+ mwa Khristu Yesu chakumasulani+ ku chilamulo cha uchimo ndi cha imfa.+