Genesis 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Motero Mulungu analenga munthu m’chifaniziro chake,+ m’chifaniziro cha Mulungu anam’lenga iye. Anawalenga mwamuna ndi mkazi.+ 1 Petulo 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 chifukwa Malemba amati: “Mukhale oyera, chifukwa ine ndine woyera.”+
27 Motero Mulungu analenga munthu m’chifaniziro chake,+ m’chifaniziro cha Mulungu anam’lenga iye. Anawalenga mwamuna ndi mkazi.+