Mateyu 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo Yesu anamuuza kuti: “Ndiwe wodala Simoni mwana wa Yona, chifukwa si munthu* amene wakuululira zimenezi, koma Atate wanga amene ali kumwamba wachita zimenezi.+
17 Pamenepo Yesu anamuuza kuti: “Ndiwe wodala Simoni mwana wa Yona, chifukwa si munthu* amene wakuululira zimenezi, koma Atate wanga amene ali kumwamba wachita zimenezi.+