Machitidwe 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atafika ku Yerusalemu+ anayesetsa kuti agwirizane ndi ophunzira kumeneko. Koma onse ankamuopa, chifukwa sanakhulupirire kuti anali wophunzira.
26 Atafika ku Yerusalemu+ anayesetsa kuti agwirizane ndi ophunzira kumeneko. Koma onse ankamuopa, chifukwa sanakhulupirire kuti anali wophunzira.