Yohane 1:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Kenako iye anapita naye kwa Yesu. Yesu atamuyang’ana+ anati: “Iwe ndiwe Simoni+ mwana wa Yohane,+ udzatchedwa Kefa” (dzina limene kumasulira kwake ndi Petulo).+ 1 Akorinto 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Panalinso zoti anaonekera kwa Kefa,+ kenako kwa atumwi 12+ aja.
42 Kenako iye anapita naye kwa Yesu. Yesu atamuyang’ana+ anati: “Iwe ndiwe Simoni+ mwana wa Yohane,+ udzatchedwa Kefa” (dzina limene kumasulira kwake ndi Petulo).+