Yohane 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti tonsefe tinalandira zinthu kuchokera pa zochuluka zimene ali nazo.+ Tinalandira kukoma mtima kwakukulu kosefukira.+ Akolose 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 chifukwa iye ndi wodzaza bwino kwambiri+ ndi makhalidwe+ a Mulungu.+
16 Pakuti tonsefe tinalandira zinthu kuchokera pa zochuluka zimene ali nazo.+ Tinalandira kukoma mtima kwakukulu kosefukira.+