Akolose 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zili motero chifukwa kunamukomera Mulungu kuti zinthu zonse+ zikhale mwa mwana wakeyo ndipo zidzazemo bwino. Akolose 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chuma chonse chokhudzana ndi nzeru ndiponso kudziwa zinthu+ chinabisidwa mosamala mwa iye. Akolose 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 chifukwa iye ndi wodzaza bwino kwambiri+ ndi makhalidwe+ a Mulungu.+
19 Zili motero chifukwa kunamukomera Mulungu kuti zinthu zonse+ zikhale mwa mwana wakeyo ndipo zidzazemo bwino.