Yohane 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti tonsefe tinalandira zinthu kuchokera pa zochuluka zimene ali nazo.+ Tinalandira kukoma mtima kwakukulu kosefukira.+ Akolose 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chuma chonse chokhudzana ndi nzeru ndiponso kudziwa zinthu+ chinabisidwa mosamala mwa iye.
16 Pakuti tonsefe tinalandira zinthu kuchokera pa zochuluka zimene ali nazo.+ Tinalandira kukoma mtima kwakukulu kosefukira.+