Aroma 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 momwemonso ifeyo, ngakhale kuti ndife ambiri, tili thupi limodzi+ mwa Khristu, ndipo aliyense payekha ndi chiwalo cha mnzake.+ Aefeso 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiponso kuti kudzera mwa mtengo wozunzikirapo*+ ayanjanitse+ magulu awiri a anthuwo kwa Mulungu, ndipo anthuwo akhale thupi limodzi,+ chifukwa anali atapheratu chidanicho+ kudzera mwa iye mwini.
5 momwemonso ifeyo, ngakhale kuti ndife ambiri, tili thupi limodzi+ mwa Khristu, ndipo aliyense payekha ndi chiwalo cha mnzake.+
16 Ndiponso kuti kudzera mwa mtengo wozunzikirapo*+ ayanjanitse+ magulu awiri a anthuwo kwa Mulungu, ndipo anthuwo akhale thupi limodzi,+ chifukwa anali atapheratu chidanicho+ kudzera mwa iye mwini.