Yohane 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo palibe munthu amene anakwera kumwamba+ koma Mwana wa munthu+ yekha, amene anatsika kuchokera kumwambako.+ Machitidwe 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Choncho pokhala mneneri, iye anaoneratu zapatsogolo ndi kuneneratu za kuuka kwa Khristu. Ananeneratu kuti iye sanasiyidwe m’Manda, komanso kuti thupi lake silinavunde.+
13 Ndipo palibe munthu amene anakwera kumwamba+ koma Mwana wa munthu+ yekha, amene anatsika kuchokera kumwambako.+
31 Choncho pokhala mneneri, iye anaoneratu zapatsogolo ndi kuneneratu za kuuka kwa Khristu. Ananeneratu kuti iye sanasiyidwe m’Manda, komanso kuti thupi lake silinavunde.+