Mateyu 12:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Pakuti monga momwe Yona+ anakhalira m’mimba mwa chinsomba chachikulu masiku atatu, usana ndi usiku, chimodzimodzinso Mwana wa munthu+ adzakhala mumtima wa dziko lapansi+ masiku atatu, usana ndi usiku.+
40 Pakuti monga momwe Yona+ anakhalira m’mimba mwa chinsomba chachikulu masiku atatu, usana ndi usiku, chimodzimodzinso Mwana wa munthu+ adzakhala mumtima wa dziko lapansi+ masiku atatu, usana ndi usiku.+