Agalatiya 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale zili choncho, pamene munali osadziwa Mulungu,+ munali akapolo a zinthu zimene mwachilengedwe si milungu.+ Aefeso 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Muzikumbukiranso kuti pa nthawi imene ija munali opanda Khristu,+ otalikirana+ ndi mtundu wa Isiraeli komanso alendo osadziwika pa mapangano a lonjezolo.+ Munalibe chiyembekezo+ ndipo inu munalibe Mulungu m’dzikoli.+ Akolose 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndithudi, inu amene kale munali otalikirana+ naye ndiponso adani ake chifukwa maganizo anu anali pa ntchito zoipa,+
8 Ngakhale zili choncho, pamene munali osadziwa Mulungu,+ munali akapolo a zinthu zimene mwachilengedwe si milungu.+
12 Muzikumbukiranso kuti pa nthawi imene ija munali opanda Khristu,+ otalikirana+ ndi mtundu wa Isiraeli komanso alendo osadziwika pa mapangano a lonjezolo.+ Munalibe chiyembekezo+ ndipo inu munalibe Mulungu m’dzikoli.+
21 Ndithudi, inu amene kale munali otalikirana+ naye ndiponso adani ake chifukwa maganizo anu anali pa ntchito zoipa,+