Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Popeza Chilamulo chinaperekedwa kudzera mwa Mose,+ kukoma mtima kwakukulu+ komanso choonadi+ zinakhalako kudzera mwa Yesu Khristu.

  • Aroma 3:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndiponso, kuyesedwa olungama chifukwa cha kukoma mtima kwake kwakukulu+ kumene wakusonyeza, powamasula ndi dipo+ lolipiridwa ndi Khristu Yesu, kuli ngati mphatso yaulere.+

  • 1 Akorinto 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Nthawi zonse ndimayamika Mulungu chifukwa cha inu, poona kukoma mtima kwakukulu+ kwa Mulungu kumene anakusonyezani kudzera mwa Khristu Yesu,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena