1 Timoteyo 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Menya nkhondo yabwino yosunga chikhulupiriro.+ Gwira mwamphamvu moyo wosatha. Anakuitanira moyo umenewu ndipo unalengeza momveka bwino+ zinthu zokhudzana ndi moyo umenewu pamaso pa mboni zambiri.
12 Menya nkhondo yabwino yosunga chikhulupiriro.+ Gwira mwamphamvu moyo wosatha. Anakuitanira moyo umenewu ndipo unalengeza momveka bwino+ zinthu zokhudzana ndi moyo umenewu pamaso pa mboni zambiri.