Afilipi 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zinthu zimene munaphunzira, zimene munazivomereza, zimene munazimva, ndi zimene munaziona kwa ine, muzichita zimenezo,+ ndipo Mulungu wamtendere+ adzakhala nanu. Tito 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 M’zinthu zonse, ukhale chitsanzo pa ntchito zabwino.+ Chiphunzitso+ chako chikhale chopanda chinyengo.+ Usonyeze kuti ndiwe wopanda chibwana. 1 Petulo 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Osati mochita ufumu+ pa anthu amene ali cholowa chochokera kwa Mulungu,+ koma mukhale zitsanzo kwa gulu la nkhosa.+
9 Zinthu zimene munaphunzira, zimene munazivomereza, zimene munazimva, ndi zimene munaziona kwa ine, muzichita zimenezo,+ ndipo Mulungu wamtendere+ adzakhala nanu.
7 M’zinthu zonse, ukhale chitsanzo pa ntchito zabwino.+ Chiphunzitso+ chako chikhale chopanda chinyengo.+ Usonyeze kuti ndiwe wopanda chibwana.
3 Osati mochita ufumu+ pa anthu amene ali cholowa chochokera kwa Mulungu,+ koma mukhale zitsanzo kwa gulu la nkhosa.+