Machitidwe 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma Ambuye anamuuza kuti: “Nyamuka uzipita, chifukwa munthu ameneyu ndi chiwiya changa chochita kusankhidwa+ chotengera dzina langa kupita nalo kwa anthu a mitundu ina,+ komanso kwa mafumu+ ndi ana a Isiraeli. Machitidwe 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndikudziwa kuti ine ndikachoka, mimbulu+ yopondereza idzafika pakati panu ndipo sidzasamalira gulu la nkhosa mwachikondi.
15 Koma Ambuye anamuuza kuti: “Nyamuka uzipita, chifukwa munthu ameneyu ndi chiwiya changa chochita kusankhidwa+ chotengera dzina langa kupita nalo kwa anthu a mitundu ina,+ komanso kwa mafumu+ ndi ana a Isiraeli.
29 Ndikudziwa kuti ine ndikachoka, mimbulu+ yopondereza idzafika pakati panu ndipo sidzasamalira gulu la nkhosa mwachikondi.