1 Akorinto 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tisakhalenso ong’ung’udza, mmene ena mwa iwo anang’ung’udzira,+ wowonongayo+ n’kuwawononga onsewo. 1 Petulo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muzicherezana popanda kudandaula.+
10 Tisakhalenso ong’ung’udza, mmene ena mwa iwo anang’ung’udzira,+ wowonongayo+ n’kuwawononga onsewo.