Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 25:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Uonetsetse kuti wazipanga motsatira chitsanzo chimene wasonyezedwa m’phiri.+

  • Aheberi 8:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma amuna amenewo akuchita utumiki wopatulikawo m’chifaniziro+ ndi mu mthunzi+ wa zinthu zakumwamba. Izi zinaonekera mu lamulo limene Mulungu anapatsa Mose, atatsala pang’ono kumanga chihema.+ Lamulo lake linali lakuti:+ “Uonetsetse kuti wapanga zinthu zonse motsatira chitsanzo chimene wasonyezedwa m’phiri.”+

  • Aheberi 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Popeza Chilamulo ndicho mthunzi chabe+ wa zinthu zabwino zimene zikubwera osati zinthu zenizenizo, ndiye kuti anthu wamba sangachititse anthu amene amalambira Mulungu kukhala angwiro. Iwo sangathe kuchita zimenezi mwa nsembe zimodzimodzizo zimene amapereka mosalekeza chaka ndi chaka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena