Yohane 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yesu anamuuza kuti: “Ine ndine njira,+ choonadi+ ndi moyo.+ Palibe amene amafika kwa Atate osadzera mwa ine.+ Aheberi 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero kunali kofunikira kuti zifaniziro+ za zinthu zakumwamba ziyeretsedwe m’njira imeneyi,+ koma zinthu zakumwamba zenizenizo ziyeretsedwe ndi nsembe zabwino kuposa nsembe zoterezi.
6 Yesu anamuuza kuti: “Ine ndine njira,+ choonadi+ ndi moyo.+ Palibe amene amafika kwa Atate osadzera mwa ine.+
23 Chotero kunali kofunikira kuti zifaniziro+ za zinthu zakumwamba ziyeretsedwe m’njira imeneyi,+ koma zinthu zakumwamba zenizenizo ziyeretsedwe ndi nsembe zabwino kuposa nsembe zoterezi.