Levitiko 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ena mwa magaziwo aziwadonthezera+ paguwalo ndi chala chake maulendo 7, kuti aliyeretse ku zodetsa za ana a Isiraeli ndi kulipatula. Levitiko 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Akamaliza kuphimbira machimo+ malo oyera, chihema chokumanako ndi guwa lansembe, azibweretsanso mbuzi yamoyo ija.+
19 Ena mwa magaziwo aziwadonthezera+ paguwalo ndi chala chake maulendo 7, kuti aliyeretse ku zodetsa za ana a Isiraeli ndi kulipatula.
20 “Akamaliza kuphimbira machimo+ malo oyera, chihema chokumanako ndi guwa lansembe, azibweretsanso mbuzi yamoyo ija.+