-
Levitiko 16:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ena mwa magaziwo aziwadonthezera paguwalo ndi chala chake maulendo 7, kuti likhale lopatulika komanso kuti aliyeretse ku zinthu zodetsa za Aisiraeli.
-