Levitiko 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ena mwa magaziwo aziwadonthezera+ paguwalo ndi chala chake maulendo 7, kuti aliyeretse ku zodetsa za ana a Isiraeli ndi kulipatula.
19 Ena mwa magaziwo aziwadonthezera+ paguwalo ndi chala chake maulendo 7, kuti aliyeretse ku zodetsa za ana a Isiraeli ndi kulipatula.