Aefeso 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Akapolo inu, muzimvera anthu amene ndi ambuye anu.+ Muziwaopa ndi kuwalemekeza+ moona mtima, monga mmene mumachitira ndi Khristu. Tito 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akapolo+ azigonjera ambuye awo pa zonse+ ndipo aziwakondweretsa. Asamatsutsane nawo+ 1 Petulo 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Antchito a panyumba akhale ogonjera+ mabwana awo ndi mantha oyenera,+ osati kwa mabwana abwino ndi ololera okha, koma ngakhalenso kwa ovuta kuwakondweretsa.
5 Akapolo inu, muzimvera anthu amene ndi ambuye anu.+ Muziwaopa ndi kuwalemekeza+ moona mtima, monga mmene mumachitira ndi Khristu.
18 Antchito a panyumba akhale ogonjera+ mabwana awo ndi mantha oyenera,+ osati kwa mabwana abwino ndi ololera okha, koma ngakhalenso kwa ovuta kuwakondweretsa.