Aefeso 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 kuphatikizapo ineyo. Chitani zimenezi kuti ndikatsegula pakamwa panga kuti ndilankhule, ndizitha kulankhula+ mwaufulu+ kuti ndidziwitse ena chinsinsi chopatulika cha uthenga wabwino,+
19 kuphatikizapo ineyo. Chitani zimenezi kuti ndikatsegula pakamwa panga kuti ndilankhule, ndizitha kulankhula+ mwaufulu+ kuti ndidziwitse ena chinsinsi chopatulika cha uthenga wabwino,+