Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Afilipi 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 N’zoyenera kwa ineyo kuganizira nonsenu mwa njira imeneyi, pakuti inu ndinu apamtima panga,+ ndiponso nonsenu ndinu ogawana+ nane m’kukoma mtima kwakukulu, m’maunyolo anga m’ndende,+ ndi pa kuteteza+ uthenga wabwino ndi kukhazikitsa mwalamulo ntchito ya uthenga wabwino.+

  • Filimoni 9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 ndikukupempha mwachikondi,+ poona mmene ndililimu. Ineyo Paulo ndine wachikulire, komanso tsopano ndine mkaidi+ chifukwa cha Khristu Yesu.

  • Aheberi 13:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kumbukirani amene ali m’ndende+ ngati kuti mwamangidwa nawo limodzi.+ Kumbukiraninso amene akuzunzidwa,+ popeza inunso mudakali m’thupi lanyama.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena