Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aefeso 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pa chifukwa chimenechi, ine Paulo, ndine wandende+ mwa Khristu Yesu m’malo mwa inu, anthu a mitundu ina+ . . .

  • Afilipi 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Moti, kumangidwa kwanga+ chifukwa cha Khristu, kwadziwika ndi aliyense+ pakati pa Asilikali Oteteza Mfumu ndi ena onse.+

  • Akolose 4:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Tsopano landirani moni wanga wolemba ndekha ndi dzanja langa,+ ineyo Paulo. Pitirizani kukumbukira maunyolo+ amene andimanga nawo kundende kuno. Kukoma mtima kwakukulu kukhale nanu.

  • 2 Timoteyo 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Chotero, usachite manyazi ndi ntchito yochitira umboni za Ambuye wathu,+ kapena za ineyo amene ndine mkaidi chifukwa cha iye.+ Khala wokonzeka kumva zowawa+ mu mphamvu ya Mulungu+ chifukwa cha uthenga wabwino.

  • Filimoni 13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndikanakonda kumusunga kuti m’malo mwa iwe,+ apitirize kunditumikira pamene ndili m’ndende+ chifukwa cha uthenga wabwino.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena