Akolose 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndikusangalala tsopano ndi masautso amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso kumbali yanga, ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira+ monga chiwalo cha thupi la Khristu, limene ndi mpingo.+ 2 Timoteyo 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Monga msilikali wabwino+ wa Khristu Yesu, khala wokonzeka kumva zowawa.+
24 Ndikusangalala tsopano ndi masautso amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso kumbali yanga, ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira+ monga chiwalo cha thupi la Khristu, limene ndi mpingo.+