Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Akorinto 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 olankhula zoona, ndiponso okhala ndi mphamvu ya Mulungu.+ Komanso, tikuchita zimenezi ponyamula zida+ za chilungamo kudzanja lamanja ndi lamanzere,

  • Afilipi 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pa zinthu zonse, ndimapeza mphamvu kuchokera kwa iye amene amandipatsa mphamvu.+

  • Akolose 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tikupemphereranso kuti mulandire mphamvu zazikulu chifukwa cha mphamvu zake zaulemerero,+ kuti muthe kupirira+ zinthu zonse ndi kukhala oleza mtima ndiponso achimwemwe,

  • 1 Petulo 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 inuyo amene Mulungu akukutetezani ndi mphamvu yake chifukwa muli ndi chikhulupiriro.+ Mulungu akukutetezani kuti mudzalandire chipulumutso,+ ndipo chipulumutso chimenechi chidzaonekera+ mu nthawi ya mapeto.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena