2 Timoteyo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho usachite manyazi ndi ntchito yolalikira za Ambuye wathu,+ kapena kuchita manyazi ndi ineyo amene ndine mkaidi chifukwa cha iye. Koma khala wokonzeka kuvutika+ chifukwa cha uthenga wabwino ndipo uzidalira mphamvu ya Mulungu.+ 2 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:8 Nsanja ya Olonda,3/1/2003, ptsa. 9-10
8 Choncho usachite manyazi ndi ntchito yolalikira za Ambuye wathu,+ kapena kuchita manyazi ndi ineyo amene ndine mkaidi chifukwa cha iye. Koma khala wokonzeka kuvutika+ chifukwa cha uthenga wabwino ndipo uzidalira mphamvu ya Mulungu.+