Aefeso 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa chifukwa chimenechi, ine Paulo, ndine wandende+ mwa Khristu Yesu m’malo mwa inu, anthu a mitundu ina+ . . . 2 Timoteyo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa cha uthengawu, ndikumva zowawa mpaka kutsekeredwa m’ndende+ ngati wochita zoipa. Komabe, mawu a Mulungu samangika.+
3 Pa chifukwa chimenechi, ine Paulo, ndine wandende+ mwa Khristu Yesu m’malo mwa inu, anthu a mitundu ina+ . . .
9 Chifukwa cha uthengawu, ndikumva zowawa mpaka kutsekeredwa m’ndende+ ngati wochita zoipa. Komabe, mawu a Mulungu samangika.+