Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 9:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pakuti ndidzamuonetsa bwinobwino zopweteka zonse zimene ayenera kumva chifukwa cha dzina langa.”+

  • Afilipi 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 N’zoyenera kwa ineyo kuganizira nonsenu mwa njira imeneyi, pakuti inu ndinu apamtima panga,+ ndiponso nonsenu ndinu ogawana+ nane m’kukoma mtima kwakukulu, m’maunyolo anga m’ndende,+ ndi pa kuteteza+ uthenga wabwino ndi kukhazikitsa mwalamulo ntchito ya uthenga wabwino.+

  • 1 Petulo 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kodi kupirira kumenyedwa mbama mutachimwa kuli ndi phindu lanji?+ Koma ngati mukupirira povutika chifukwa cha kuchita zabwino,+ zimenezo n’zabwino kwa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena