2 Timoteyo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa cha uthengawu, ndikuvutika ndipo ndatsekeredwa mʼndende ngati chigawenga.+ Komabe mawu a Mulungu samangika.+
9 Chifukwa cha uthengawu, ndikuvutika ndipo ndatsekeredwa mʼndende ngati chigawenga.+ Komabe mawu a Mulungu samangika.+