Yohane 12:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pamene kuwala mudakali nako, sonyezani chikhulupiriro mwa kuwalako, kuti mukhale ana ake a kuwala.”+ Yesu atanena zimenezi, anachoka ndi kuwabisalira.
36 Pamene kuwala mudakali nako, sonyezani chikhulupiriro mwa kuwalako, kuti mukhale ana ake a kuwala.”+ Yesu atanena zimenezi, anachoka ndi kuwabisalira.