Aroma 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choyamba, ndikuyamika+ Mulungu wanga kudzera mwa Yesu Khristu chifukwa cha nonsenu, pakuti chikhulupiriro chanu chikusimbidwa+ m’dziko lonse. Aroma 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma ndifunsebe kuti, Kodi kumva sanamve? Pajatu “liwu lawo linamveka padziko lonse lapansi,+ ndipo mawu awo anamveka kumalekezero a dziko lapansi kumene kuli anthu.”+
8 Choyamba, ndikuyamika+ Mulungu wanga kudzera mwa Yesu Khristu chifukwa cha nonsenu, pakuti chikhulupiriro chanu chikusimbidwa+ m’dziko lonse.
18 Koma ndifunsebe kuti, Kodi kumva sanamve? Pajatu “liwu lawo linamveka padziko lonse lapansi,+ ndipo mawu awo anamveka kumalekezero a dziko lapansi kumene kuli anthu.”+