Machitidwe 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho mwachizolowezi chake,+ Paulo analowa m’sunagogemo, ndipo kwa masabata atatu anakambirana nawo mfundo za m’Malemba.+
2 Choncho mwachizolowezi chake,+ Paulo analowa m’sunagogemo, ndipo kwa masabata atatu anakambirana nawo mfundo za m’Malemba.+