Afilipi 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo ndili pamodzi ndi Timoteyo monga akapolo+ a Khristu Yesu. Ndikulembera oyera onse ogwirizana ndi Khristu Yesu amene ali ku Filipi,+ komanso oyang’anira ndi atumiki othandiza:+
1 Ine Paulo ndili pamodzi ndi Timoteyo monga akapolo+ a Khristu Yesu. Ndikulembera oyera onse ogwirizana ndi Khristu Yesu amene ali ku Filipi,+ komanso oyang’anira ndi atumiki othandiza:+