Aefeso 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chotero, simulinso anthu osadziwika+ kapena alendo m’dziko la eni,+ koma ndinu nzika+ zinzawo za oyerawo,+ ndipo ndinu a m’banja+ la Mulungu. Aheberi 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma Khristu monga Mwana+ wa mwiniwake wa nyumbayo, anali kuyang’anira nyumba ya Mulungu mokhulupirika. Ife ndife nyumba ya Mulunguyo,+ ngati tagwira mwamphamvu ufulu wathu wa kulankhula ndi kupitirizabe kunyadira chiyembekezocho mpaka mapeto.+
19 Chotero, simulinso anthu osadziwika+ kapena alendo m’dziko la eni,+ koma ndinu nzika+ zinzawo za oyerawo,+ ndipo ndinu a m’banja+ la Mulungu.
6 Koma Khristu monga Mwana+ wa mwiniwake wa nyumbayo, anali kuyang’anira nyumba ya Mulungu mokhulupirika. Ife ndife nyumba ya Mulunguyo,+ ngati tagwira mwamphamvu ufulu wathu wa kulankhula ndi kupitirizabe kunyadira chiyembekezocho mpaka mapeto.+