Akolose 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo kalatayi mukaiwerenga kwanuko, konzani zoti ikawerengedwenso+ ku mpingo wa Alaodikaya, ndiponso mukawerenge yochokera ku Laodikaya. 1 Atesalonika 5:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndikukulamulani mwa Ambuye kuti kalatayi iwerengedwe kwa abale onse.+
16 Ndipo kalatayi mukaiwerenga kwanuko, konzani zoti ikawerengedwenso+ ku mpingo wa Alaodikaya, ndiponso mukawerenge yochokera ku Laodikaya.