Miyambo 23:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mvera bambo ako amene anakubereka,+ ndipo usanyoze mayi ako chifukwa chakuti akalamba.+