1 Samueli 25:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Nthawi yomweyo, ananyamuka ndi kugwada mpaka nkhope yake pansi,+ n’kunena kuti: “Ine kapolo wanu ndine wokonzeka kukhala mtumiki wosambitsa mapazi+ a atumiki a mbuyanga.”+ Yohane 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atatero anathira madzi m’beseni ndi kuyamba kusambitsa mapazi+ a ophunzira ndi kuwapukuta ndi thaulo limene anamanga m’chiuno lija. Yohane 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho ngati ine, wokhala Ambuye ndi Mphunzitsi, ndasambitsa mapazi anu,+ inunso muyenera kusambitsana mapazi.+
41 Nthawi yomweyo, ananyamuka ndi kugwada mpaka nkhope yake pansi,+ n’kunena kuti: “Ine kapolo wanu ndine wokonzeka kukhala mtumiki wosambitsa mapazi+ a atumiki a mbuyanga.”+
5 Atatero anathira madzi m’beseni ndi kuyamba kusambitsa mapazi+ a ophunzira ndi kuwapukuta ndi thaulo limene anamanga m’chiuno lija.
14 Choncho ngati ine, wokhala Ambuye ndi Mphunzitsi, ndasambitsa mapazi anu,+ inunso muyenera kusambitsana mapazi.+