Mateyu 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano Yesu anaimirira pamaso pa bwanamkubwa, ndipo bwanamkubwayo anamufunsa kuti: “Kodi ndiwe mfumu ya Ayuda?”+ Yesu anayankha kuti: “Mukunena nokha.”+
11 Tsopano Yesu anaimirira pamaso pa bwanamkubwa, ndipo bwanamkubwayo anamufunsa kuti: “Kodi ndiwe mfumu ya Ayuda?”+ Yesu anayankha kuti: “Mukunena nokha.”+