Mateyu 26:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Yesu anamuyankha+ kuti: “Mwanena nokha.+ Ndipo ndikukuuzani anthu inu kuti, kuyambira tsopano+ mudzaona Mwana wa munthu+ atakhala kudzanja lamanja+ lamphamvu. Mudzamuonanso akubwera pamitambo yakumwamba.”+ 1 Timoteyo 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamaso pa Mulungu, amene amasunga zinthu zonse kuti zikhalebe zamoyo, ndi pamaso pa Khristu Yesu, amene anapereka umboni wabwino kwambiri+ pamaso pa Pontiyo Pilato,+ ndikukulamula+
64 Yesu anamuyankha+ kuti: “Mwanena nokha.+ Ndipo ndikukuuzani anthu inu kuti, kuyambira tsopano+ mudzaona Mwana wa munthu+ atakhala kudzanja lamanja+ lamphamvu. Mudzamuonanso akubwera pamitambo yakumwamba.”+
13 Pamaso pa Mulungu, amene amasunga zinthu zonse kuti zikhalebe zamoyo, ndi pamaso pa Khristu Yesu, amene anapereka umboni wabwino kwambiri+ pamaso pa Pontiyo Pilato,+ ndikukulamula+