Agalatiya 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma iwo ataona kuti ndapatsidwa+ ntchito yolalikira uthenga wabwino kwa anthu osadulidwa,+ mmene Petulo anapatsidwira ntchito yoti akalalikire uthenga wabwino kwa anthu odulidwa,+ Akolose 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndinakhala mtumiki+ wa mpingo umenewu mogwirizana ndi udindo+ umene Mulungu anandipatsa, woti ndilalikire mawu a Mulungu mokwanira, kuti inuyo mupindule. 1 Atesalonika 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma popeza Mulungu wationa kuti ndife oyenera kupatsidwa+ ntchito yolalikira uthenga wabwino, tikulankhula monga anthu okondweretsa+ Mulungu, yemwe amavomereza mitima+ yathu, osati monga okondweretsa anthu.
7 Koma iwo ataona kuti ndapatsidwa+ ntchito yolalikira uthenga wabwino kwa anthu osadulidwa,+ mmene Petulo anapatsidwira ntchito yoti akalalikire uthenga wabwino kwa anthu odulidwa,+
25 Ndinakhala mtumiki+ wa mpingo umenewu mogwirizana ndi udindo+ umene Mulungu anandipatsa, woti ndilalikire mawu a Mulungu mokwanira, kuti inuyo mupindule.
4 Koma popeza Mulungu wationa kuti ndife oyenera kupatsidwa+ ntchito yolalikira uthenga wabwino, tikulankhula monga anthu okondweretsa+ Mulungu, yemwe amavomereza mitima+ yathu, osati monga okondweretsa anthu.